Yesaya 61:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inuyo mudzatchedwa ansembe a Yehova.+Anthu adzakutchulani kuti atumiki a Mulungu wathu. Mudzadya zinthu zochokera kumitundu ya anthu+Ndiponso mudzadzitamandira chifukwa cha ulemerero umene* mudzapeze kuchokera kwa iwo.
6 Inuyo mudzatchedwa ansembe a Yehova.+Anthu adzakutchulani kuti atumiki a Mulungu wathu. Mudzadya zinthu zochokera kumitundu ya anthu+Ndiponso mudzadzitamandira chifukwa cha ulemerero umene* mudzapeze kuchokera kwa iwo.