-
Ezekieli 36:33, 34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Pa tsiku limene ndidzakuyeretseni nʼkuchotsa zolakwa zanu zonse, ndidzachititsa kuti mʼmizinda yanu muzikhala anthu+ komanso kuti malo amene anali mabwinja amangidwenso.+ 34 Anthu adzalima mʼdziko limene linawonongedwa, limene aliyense wodutsa ankaliona kuti ndi bwinja.
-