Zekariya 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndidzawabweretsa, ndipo azidzakhala mu Yerusalemu.+ Iwo adzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo+ woona* ndi wachilungamo.’”
8 Ndidzawabweretsa, ndipo azidzakhala mu Yerusalemu.+ Iwo adzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo+ woona* ndi wachilungamo.’”