Deuteronomo 28:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mudzalonjeza kukwatira mkazi koma mwamuna wina adzamugwiririra. Mudzamanga nyumba koma simudzakhalamo.+ Mudzadzala mitengo ya mpesa koma simudzadya zipatso zake.+ Hoseya 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo akungofesa mphepo,Ndipo adzakolola mphepo yamkuntho.+ Mbewu zawo sizidzakula mpaka kukhwima.+Ndipo zimene zidzakule, sizidzawapatsa ufa. Ngati zina zingabereke, alendo adzazimeza.+
30 Mudzalonjeza kukwatira mkazi koma mwamuna wina adzamugwiririra. Mudzamanga nyumba koma simudzakhalamo.+ Mudzadzala mitengo ya mpesa koma simudzadya zipatso zake.+
7 Iwo akungofesa mphepo,Ndipo adzakolola mphepo yamkuntho.+ Mbewu zawo sizidzakula mpaka kukhwima.+Ndipo zimene zidzakule, sizidzawapatsa ufa. Ngati zina zingabereke, alendo adzazimeza.+