Ezekieli 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zopalasira zako anazipanga ndi mitengo ikuluikulu ya ku Basana,Ndipo mbali yakutsogolo kwako anaipanga ndi matabwa a paini, nʼkuikongoletsa ndi minyanga yochokera kuzilumba za Kitimu.+
6 Zopalasira zako anazipanga ndi mitengo ikuluikulu ya ku Basana,Ndipo mbali yakutsogolo kwako anaipanga ndi matabwa a paini, nʼkuikongoletsa ndi minyanga yochokera kuzilumba za Kitimu.+