Deuteronomo 32:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndikanola lupanga langa lonyezimira,Nʼkukonzekeretsa dzanja langa kuti lipereke chiweruzo,+Ndidzabwezera adani anga,+Ndipo ndidzapereka chilango kwa amene amadana nane. Yeremiya 47:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aa! iwe lupanga la Yehova.+ Kodi sukhala chete mpaka liti? Bwerera mʼchimake. Upume ndipo ukhale chete.
41 Ndikanola lupanga langa lonyezimira,Nʼkukonzekeretsa dzanja langa kuti lipereke chiweruzo,+Ndidzabwezera adani anga,+Ndipo ndidzapereka chilango kwa amene amadana nane.
6 Aa! iwe lupanga la Yehova.+ Kodi sukhala chete mpaka liti? Bwerera mʼchimake. Upume ndipo ukhale chete.