Yeremiya 47:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Eyaa! iwe lupanga la Yehova.+ Kodi sukhala chete kufikira liti? Bwerera m’chimake.+ Pumula, ndipo ukhale chete.
6 “Eyaa! iwe lupanga la Yehova.+ Kodi sukhala chete kufikira liti? Bwerera m’chimake.+ Pumula, ndipo ukhale chete.