Yeremiya 47:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aa! iwe lupanga la Yehova.+ Kodi sukhala chete mpaka liti? Bwerera mʼchimake. Upume ndipo ukhale chete.
6 Aa! iwe lupanga la Yehova.+ Kodi sukhala chete mpaka liti? Bwerera mʼchimake. Upume ndipo ukhale chete.