Salimo 80:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Munachititsa kuti mtengo wa mpesa+ uchoke mu Iguputo. Munathamangitsa mitundu ya anthu kuti mudzalemo mtengowo.+ Yesaya 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikufuna ndimuimbire nyimbo wokondedwa wangaNyimbo yonena za munthu amene ndimamukonda ndiponso munda wake wa mpesa.+ Wokondedwa wanga anali ndi munda wa mpesa pamalo achonde mʼmbali mwa phiri. Yeremiya 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ine ndinakudzala ngati mtengo wa mpesa wofiira,+ wabwino kwambiri umene unamera kuchokera ku mbewu yabwino kwambiri.Ndiye wandisinthira bwanji nʼkukhala mphukira zachabechabe za mtengo wa mpesa wachilendo?’+
8 Munachititsa kuti mtengo wa mpesa+ uchoke mu Iguputo. Munathamangitsa mitundu ya anthu kuti mudzalemo mtengowo.+
5 Ndikufuna ndimuimbire nyimbo wokondedwa wangaNyimbo yonena za munthu amene ndimamukonda ndiponso munda wake wa mpesa.+ Wokondedwa wanga anali ndi munda wa mpesa pamalo achonde mʼmbali mwa phiri.
21 Ine ndinakudzala ngati mtengo wa mpesa wofiira,+ wabwino kwambiri umene unamera kuchokera ku mbewu yabwino kwambiri.Ndiye wandisinthira bwanji nʼkukhala mphukira zachabechabe za mtengo wa mpesa wachilendo?’+