Salimo 103:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye sadzakhalira kutipezera zifukwa nthawi zonse,+Kapena kutisungira mkwiyo mpaka kalekale.+ Yesaya 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu anthu anga amene mwapunthidwa ngati mbewu,Mbewu zapamalo* anga opunthira,+Ndakuuzani zonse zimene ndamva kwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli. Mika 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu,Amene amakhululukira zolakwa ndi machimo+ a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale,Chifukwa mumakonda chikondi chokhulupirika.+
10 Inu anthu anga amene mwapunthidwa ngati mbewu,Mbewu zapamalo* anga opunthira,+Ndakuuzani zonse zimene ndamva kwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli.
18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu,Amene amakhululukira zolakwa ndi machimo+ a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale,Chifukwa mumakonda chikondi chokhulupirika.+