Yesaya 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu anthu anga amene mwapunthidwa ngati mbewu, ndi iwe mwana wa pamalo anga opunthira mbewu,+ zimene ndamva kwa Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, n’zimene ndakuuzani anthu inu. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:10 Yesaya 1, ptsa. 224-225
10 Inu anthu anga amene mwapunthidwa ngati mbewu, ndi iwe mwana wa pamalo anga opunthira mbewu,+ zimene ndamva kwa Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, n’zimene ndakuuzani anthu inu.