Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 8:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 “Anthu anu akakuchimwirani+ (popeza palibe munthu amene sachimwa)+ inu n’kuwakwiyira, n’kuwapereka kwa adani, adani awowo n’kuwagwira kupita nawo kudziko la adani, lakutali kapena lapafupi,+

  • 2 Mafumu 13:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Yehoahazi sanatsale ndi anthu alionse kupatulapo amuna 50 okwera pamahatchi, magaleta 10, ndi asilikali 10,000 oyenda pansi,+ chifukwa mfumu ya Siriya inawawononga+ ndi kuwapondaponda ngati fumbi la popunthira mbewu.+

  • Yesaya 1:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndidzakutembenuzirani dzanja langa. Ndidzasungunula zonyansa zanu zonse, ndipo ndidzachotsa nyansi zanu zonse.+

  • Mateyu 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Fosholo yake youluzira mankhusu* ili m’manja mwake, ndipo malo ake opunthirapo mbewu adzawayeretseratu kuti mbee! Tirigu adzamututira m’nkhokwe,+ koma mankhusu adzawatentha+ ndi moto umene sungazimitsidwe.”

  • Aheberi 12:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pakuti Yehova amalanga aliyense amene iye amamukonda, ndipo amakwapula aliyense amene iye amamulandira monga mwana wake.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena