Yesaya 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu anthu anga amene mwapunthidwa ngati mbewu,Mbewu zapamalo* anga opunthira,+Ndakuuzani zonse zimene ndamva kwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:10 Yesaya 1, ptsa. 224-225
10 Inu anthu anga amene mwapunthidwa ngati mbewu,Mbewu zapamalo* anga opunthira,+Ndakuuzani zonse zimene ndamva kwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli.