2 Mafumu 19:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Yesaya mwana wa Amozi anatumiza uthenga kwa Hezekiya, wakuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndamva pemphero lako+ lokhudza Senakeribu mfumu ya Asuri.+ Yesaya 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Masomphenya amene Yesaya*+ mwana wa Amozi anaona, okhudza Yuda ndi Yerusalemu mʼmasiku a Uziya,+ Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya,+ mafumu a Yuda:+
20 Ndiyeno Yesaya mwana wa Amozi anatumiza uthenga kwa Hezekiya, wakuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndamva pemphero lako+ lokhudza Senakeribu mfumu ya Asuri.+
1 Masomphenya amene Yesaya*+ mwana wa Amozi anaona, okhudza Yuda ndi Yerusalemu mʼmasiku a Uziya,+ Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya,+ mafumu a Yuda:+