Salimo 39:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Imvani pemphero langa, inu Yehova,Mvetserani pamene ndikulira kupempha thandizo.+ Musanyalanyaze misozi yanga. Chifukwa ndine mlendo kwa inu,+Mlendo wongodutsa mofanana ndi makolo anga onse.+ Salimo 119:82 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 82 Maso anga akulakalaka mawu anu+Ndipo ndikunena kuti: “Kodi mudzandilimbikitsa liti?”+ Salimo 119:123 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 123 Maso anga afooka chifukwa choyembekezera chipulumutso chanu+Komanso malonjezo* anu olungama.+
12 Imvani pemphero langa, inu Yehova,Mvetserani pamene ndikulira kupempha thandizo.+ Musanyalanyaze misozi yanga. Chifukwa ndine mlendo kwa inu,+Mlendo wongodutsa mofanana ndi makolo anga onse.+