1 Samueli 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova amapha komanso amasunga moyo,*Iye amatsitsira Kumanda* komanso amaukitsa.+ Yobu 33:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iye wandiwombola* kuti ndisapite kudzenje,*+Ndipo moyo wanga udzaona kuwala.’ Salimo 71:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ngakhale kuti mwachititsa kuti ndikumane ndi mavuto komanso masoka ambiri,+Bwezeretsani mphamvu zanga.Nditulutseni mʼdzenje lakuya.*+
20 Ngakhale kuti mwachititsa kuti ndikumane ndi mavuto komanso masoka ambiri,+Bwezeretsani mphamvu zanga.Nditulutseni mʼdzenje lakuya.*+