Yesaya 46:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kutatsala nthawi yaitali, ndimaneneratu zimene zidzachitike,Ndipo kale kwambiri ndinaneneratu zinthu zimene zidzachitike mʼtsogolo.+ Ine ndimanena kuti, ‘Zolinga zanga zidzachitikadi,+Ndipo ndidzachita chilichonse chimene ndikufuna.’+ 1 Petulo 1:24, 25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti “anthu onse ali ngati udzu, ndipo ulemerero wawo wonse uli ngati duwa lakutchire. Udzu umafota ndipo duwa limathothoka, 25 koma mawu a Yehova* adzakhalapo mpaka kalekale.”+ “Mawu” amenewa ndi uthenga wabwino umene unalengezedwa kwa inu.+
10 Kutatsala nthawi yaitali, ndimaneneratu zimene zidzachitike,Ndipo kale kwambiri ndinaneneratu zinthu zimene zidzachitike mʼtsogolo.+ Ine ndimanena kuti, ‘Zolinga zanga zidzachitikadi,+Ndipo ndidzachita chilichonse chimene ndikufuna.’+
24 Pakuti “anthu onse ali ngati udzu, ndipo ulemerero wawo wonse uli ngati duwa lakutchire. Udzu umafota ndipo duwa limathothoka, 25 koma mawu a Yehova* adzakhalapo mpaka kalekale.”+ “Mawu” amenewa ndi uthenga wabwino umene unalengezedwa kwa inu.+