2 Samueli 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Anthu onse amʼdzikoli ankalira mokweza mawu, pamene anthu onse amene anali ndi Davide ankadutsa. Mfumu inali itaimirira pafupi ndi chigwa cha Kidironi+ ndipo anthu onse ankawoloka kulowera kumsewu wopita kuchipululu. 2 Mafumu 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mfumuyo inatulutsa mzati* wopatulika+ umene unali mʼnyumba ya Yehova ndipo inapita nawo kuchigwa cha Kidironi kunja kwa mzinda wa Yerusalemu nʼkukautentha.+ Itatero, inauperapera nʼkuwaza fumbi lake pamanda a anthu wamba.+ Yohane 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Atamaliza kunena zinthu zimenezi, Yesu anatuluka limodzi ndi ophunzira ake nʼkuwoloka chigwa cha Kidironi+ kupita kumene kunali munda. Iye ndi ophunzira akewo analowa mʼmundamo.+
23 Anthu onse amʼdzikoli ankalira mokweza mawu, pamene anthu onse amene anali ndi Davide ankadutsa. Mfumu inali itaimirira pafupi ndi chigwa cha Kidironi+ ndipo anthu onse ankawoloka kulowera kumsewu wopita kuchipululu.
6 Mfumuyo inatulutsa mzati* wopatulika+ umene unali mʼnyumba ya Yehova ndipo inapita nawo kuchigwa cha Kidironi kunja kwa mzinda wa Yerusalemu nʼkukautentha.+ Itatero, inauperapera nʼkuwaza fumbi lake pamanda a anthu wamba.+
18 Atamaliza kunena zinthu zimenezi, Yesu anatuluka limodzi ndi ophunzira ake nʼkuwoloka chigwa cha Kidironi+ kupita kumene kunali munda. Iye ndi ophunzira akewo analowa mʼmundamo.+