-
Yeremiya 36:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Yehudi akawerenga zigawo zitatu kapena 4 za mpukutuwo, mfumu inkadula mpukutuwo ndi mpeni wa mlembi nʼkuponya chidutswacho pamoto umene unali mʼmbaula uja. Inachita izi mpaka mpukutu wonsewo unathera pamotopo.
-