2 Mbiri 35:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pambuyo pa zonsezi, Yosiya atakonza kachisi, Neko+ mfumu ya Iguputo anabwera kudzamenya nkhondo ku Karikemisi pafupi ndi mtsinje wa Firate, ndipo Yosiya anapita kukamenyana naye.+
20 Pambuyo pa zonsezi, Yosiya atakonza kachisi, Neko+ mfumu ya Iguputo anabwera kudzamenya nkhondo ku Karikemisi pafupi ndi mtsinje wa Firate, ndipo Yosiya anapita kukamenyana naye.+