2 Mbiri 35:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pambuyo pa zonsezi, Yosiya atakonza nyumba ya Mulungu, Neko+ mfumu ya Iguputo+ anabwera kudzachita nkhondo ku Karikemisi+ pafupi ndi mtsinje wa Firate, ndipo Yosiya+ anapita kukakumana naye.+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 35:20 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2017, tsa. 27
20 Pambuyo pa zonsezi, Yosiya atakonza nyumba ya Mulungu, Neko+ mfumu ya Iguputo+ anabwera kudzachita nkhondo ku Karikemisi+ pafupi ndi mtsinje wa Firate, ndipo Yosiya+ anapita kukakumana naye.+