2 Mafumu 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 M’masiku ake, Farao Neko+ mfumu ya Iguputo inabwera kudzathandiza mfumu ya Asuri pamtsinje wa Firate,+ ndipo Mfumu Yosiya inapita kukamenyana ndi mfumu ya Iguputoyo,+ koma mfumuyo inapha Yosiya+ ku Megido+ itangomuona. Miyambo 3:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Usakangane ndi munthu popanda chifukwa,+ ngati sanakuchitire choipa.+ Miyambo 26:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Munthu wongodutsa amene amalowerera mkangano womwe si wake n’kukwiya nawo, ali ngati munthu wogwira makutu a galu.+
29 M’masiku ake, Farao Neko+ mfumu ya Iguputo inabwera kudzathandiza mfumu ya Asuri pamtsinje wa Firate,+ ndipo Mfumu Yosiya inapita kukamenyana ndi mfumu ya Iguputoyo,+ koma mfumuyo inapha Yosiya+ ku Megido+ itangomuona.
17 Munthu wongodutsa amene amalowerera mkangano womwe si wake n’kukwiya nawo, ali ngati munthu wogwira makutu a galu.+