2 Mbiri 35:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pambuyo pa zonsezi, Yosiya atakonza nyumba ya Mulungu, Neko+ mfumu ya Iguputo+ anabwera kudzachita nkhondo ku Karikemisi+ pafupi ndi mtsinje wa Firate, ndipo Yosiya+ anapita kukakumana naye.+ Miyambo 26:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Munthu wongodutsa amene amalowerera mkangano womwe si wake n’kukwiya nawo, ali ngati munthu wogwira makutu a galu.+ Luka 14:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kapena ndi mfumu yanji, imene popita kukakumana ndi mfumu inzake pa nkhondo, siyamba yakhala pansi ndi kuganiza mofatsa ngati asilikali ake 10,000 angathe kulimbana ndi asilikali 20,000 a mfumu yobwera kudzalimbana naye?+
20 Pambuyo pa zonsezi, Yosiya atakonza nyumba ya Mulungu, Neko+ mfumu ya Iguputo+ anabwera kudzachita nkhondo ku Karikemisi+ pafupi ndi mtsinje wa Firate, ndipo Yosiya+ anapita kukakumana naye.+
17 Munthu wongodutsa amene amalowerera mkangano womwe si wake n’kukwiya nawo, ali ngati munthu wogwira makutu a galu.+
31 Kapena ndi mfumu yanji, imene popita kukakumana ndi mfumu inzake pa nkhondo, siyamba yakhala pansi ndi kuganiza mofatsa ngati asilikali ake 10,000 angathe kulimbana ndi asilikali 20,000 a mfumu yobwera kudzalimbana naye?+