Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 29:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Umuuze kuti: ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti:

      “Ine ndikulanga iwe Farao mfumu ya Iguputo,+

      Iwe chilombo chachikulu chamʼnyanja chimene chagona mʼngalande zotuluka mumtsinje wake wa Nailo,+

      Ndipo wanena kuti, ‘Mtsinje wa Nailo ndi wanga.

      Ineyo ndinaupanga ndekha.’+

  • Ezekieli 32:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Iwe mwana wa munthu, imba nyimbo yoimba polira yokhudza Farao, mfumu ya Iguputo ndipo umuuze kuti,

      ‘Iwe unali ngati mkango waungʼono wamphamvu* wa mitundu ina ya anthu,

      Koma wakhalitsidwa chete.

      Unali ngati chilombo chamʼnyanja+ chimene chimavundula madzi mwamphamvu mʼmitsinje yako

      Nʼkumadetsa madzi ndi mapazi ako ndiponso kuipitsa mitsinjeyo.’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena