-
Yesaya 16:8, 9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Chifukwa minda yamʼmapiri ya ku Hesiboni+ yafota,
Chimodzimodzinso mitengo ya mpesa ya ku Sibima,+
Olamulira anthu a mitundu ina apondaponda nthambi zake zofiira kwambiri.*
Nthambizo zinafika mpaka ku Yazeri,+
Zinafika mpaka kuchipululu.
Mphukira zake zinakula mpaka zinafika kunyanja.
9 Nʼchifukwa chake ndidzalirire mtengo wa mpesa wa ku Sibima pamene ndikulirira Yazeri.
-
-
Yeremiya 48:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Chigwa chidzawonongedwa,
Chimodzimodzinso malo afulati,* mogwirizana ndi zimene Yehova wanena.
-