-
Yesaya 16:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 chifukwa minda ya m’mapiri ya ku Hesiboni+ yafota. Eni ake a mitundu ya anthu athyola nthambi za mitengo ya mpesa ya ku Sibima+ zodzaza ndi mphesa zakupsa. Nthambizo zinafika mpaka ku Yazeri.+ Zinafika mpaka kuchipululu. Mphukira zake zinasiyidwa kuti zizingodzikulira pazokha. Zinafika mpaka kunyanja.
-