Numeri 32:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Midzi ya Ataroti,+ Diboni,+ Yazeri, Nimira,+ Hesiboni,+ Eleyale,+ Sebamu, Nebo,+ ndi Beoni,+ Yoswa 13:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Gawo lawo linayambira kumzinda wa Yazeri,+ mizinda yonse ya ku Giliyadi,+ ndi hafu ya dziko la ana a Amoni,+ mpaka kukafika ku Aroweli+ kufupi ndi Raba.+ Yeremiya 48:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “‘Iwe mtengo wa mpesa wa ku Sibima+ ndidzakulirira kuposa mmene ndingalirire Yazeri.+ Mphukira zako zosangalala zawoloka nyanja. Zafika kunyanja, ku Yazeri.+ Munthu wofunkha waukira zipatso zako za m’chilimwe*+ ndi mphesa zimene wakolola.+
25 Gawo lawo linayambira kumzinda wa Yazeri,+ mizinda yonse ya ku Giliyadi,+ ndi hafu ya dziko la ana a Amoni,+ mpaka kukafika ku Aroweli+ kufupi ndi Raba.+
32 “‘Iwe mtengo wa mpesa wa ku Sibima+ ndidzakulirira kuposa mmene ndingalirire Yazeri.+ Mphukira zako zosangalala zawoloka nyanja. Zafika kunyanja, ku Yazeri.+ Munthu wofunkha waukira zipatso zako za m’chilimwe*+ ndi mphesa zimene wakolola.+