Numeri 32:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ana a Rubeni anamanga mizinda ya Hesiboni,+ Eleyale,+ Kiriyataimu,+ Yeremiya 48:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “‘Kulira kochokera ku Hesiboni+ kudzamveka ku Eleyale+ ndi ku Yahazi.+ Kulira kochokera ku Zowari+ kudzamveka ku Horonaimu+ ndi ku Egilati-selisiya.+ Madzi a ku Nimurimu+ nawonso adzawonongedwa.
34 “‘Kulira kochokera ku Hesiboni+ kudzamveka ku Eleyale+ ndi ku Yahazi.+ Kulira kochokera ku Zowari+ kudzamveka ku Horonaimu+ ndi ku Egilati-selisiya.+ Madzi a ku Nimurimu+ nawonso adzawonongedwa.