Numeri 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho Aisiraeli analanda mizinda yonseyi n’kuyamba kukhala m’mizinda yonse ya Aamori+ ku Hesiboni,+ ndi m’midzi yake yonse yozungulira. Yoswa 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Hesiboni,+ ndi midzi yake yonse+ imene inali m’malo okwererapowo. Linaphatikizaponso Diboni,+ Bamoti-baala,+ Beti-baala-meoni,+ Yeremiya 48:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mowabu sakutamandidwanso.+ Anthu a ku Hesiboni+ amukonzera chiwembu ndipo akunena kuti: ‘Bwerani amuna inu, tiyeni tifafanize Mowabu kuti asakhalenso mtundu wa anthu.’+ “Inunso anthu a ku Madimeni khalani chete. Lupanga likukutsatirani.
25 Choncho Aisiraeli analanda mizinda yonseyi n’kuyamba kukhala m’mizinda yonse ya Aamori+ ku Hesiboni,+ ndi m’midzi yake yonse yozungulira.
17 Hesiboni,+ ndi midzi yake yonse+ imene inali m’malo okwererapowo. Linaphatikizaponso Diboni,+ Bamoti-baala,+ Beti-baala-meoni,+
2 Mowabu sakutamandidwanso.+ Anthu a ku Hesiboni+ amukonzera chiwembu ndipo akunena kuti: ‘Bwerani amuna inu, tiyeni tifafanize Mowabu kuti asakhalenso mtundu wa anthu.’+ “Inunso anthu a ku Madimeni khalani chete. Lupanga likukutsatirani.