Deuteronomo 2:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Kenako, ndinatumiza amithenga a mawu amtendere+ kuchokera m’chipululu cha Kademoti,+ kupita kwa Sihoni+ mfumu ya Hesiboni, kuti, Oweruza 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Kenako Aisiraeli anatumiza mithenga kwa Sihoni mfumu ya Aamori, ya ku Hesiboni,+ kuti: “Tiloleni tidutse m’dziko lanu kupita kumalo athu.”+ Nyimbo ya Solomo 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Khosi lako+ lili ngati nsanja ya mnyanga wa njovu. Maso ako+ ali ngati maiwe a ku Hesiboni,+ amene ali pafupi ndi chipata cha Bati-rabimu. Mphuno yako ili ngati nsanja ya Lebanoni, imene inayang’ana cha ku Damasiko.
26 “Kenako, ndinatumiza amithenga a mawu amtendere+ kuchokera m’chipululu cha Kademoti,+ kupita kwa Sihoni+ mfumu ya Hesiboni, kuti,
19 “‘Kenako Aisiraeli anatumiza mithenga kwa Sihoni mfumu ya Aamori, ya ku Hesiboni,+ kuti: “Tiloleni tidutse m’dziko lanu kupita kumalo athu.”+
4 Khosi lako+ lili ngati nsanja ya mnyanga wa njovu. Maso ako+ ali ngati maiwe a ku Hesiboni,+ amene ali pafupi ndi chipata cha Bati-rabimu. Mphuno yako ili ngati nsanja ya Lebanoni, imene inayang’ana cha ku Damasiko.