Nyimbo ya Solomo 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Khosi lako+ lili ngati nsanja ya mnyanga wa njovu.+ Maso ako+ ali ngati madamu a madzi a ku Hesiboni,+Amene ali pafupi ndi geti la Bati-rabimu. Mphuno yako ili ngati nsanja ya ku Lebanoni,Imene inayangʼana cha ku Damasiko. Nyimbo ya Solomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:4 Nsanja ya Olonda,11/15/2006, tsa. 2011/15/1987, tsa. 25
4 Khosi lako+ lili ngati nsanja ya mnyanga wa njovu.+ Maso ako+ ali ngati madamu a madzi a ku Hesiboni,+Amene ali pafupi ndi geti la Bati-rabimu. Mphuno yako ili ngati nsanja ya ku Lebanoni,Imene inayangʼana cha ku Damasiko.