Nyimbo ya Solomo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Masaya ako ndi okongola pakati pa tsitsi lako lomanga, ndipo khosi lako lovala mkandalo limaoneka bwino.+ Nyimbo ya Solomo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Khosi lako+ lili ngati nsanja+ ya Davide. Lili ngati nsanja yomangidwa ndi miyala yokhala m’mizeremizere, yomwe akolekapo zishango 1,000, zishango zonse zozungulira+ za amuna amphamvu.
10 Masaya ako ndi okongola pakati pa tsitsi lako lomanga, ndipo khosi lako lovala mkandalo limaoneka bwino.+
4 Khosi lako+ lili ngati nsanja+ ya Davide. Lili ngati nsanja yomangidwa ndi miyala yokhala m’mizeremizere, yomwe akolekapo zishango 1,000, zishango zonse zozungulira+ za amuna amphamvu.