Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 3:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndiyeno Palali mwana wamwamuna wa Uzai, anakonza mpandawo kutsogolo kwa Mchirikizo wa Khoma ndipo anakonzanso nsanja yochokera pa Nyumba ya Mfumu+ imene ili kumtunda m’Bwalo la Alonda.+ Kenako, Pedaya mwana wamwamuna wa Parosi,+ anakonza mpandawo kuchokera pamene Palali analekezera.

  • Nyimbo ya Solomo 7:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Khosi lako+ lili ngati nsanja ya mnyanga wa njovu. Maso ako+ ali ngati maiwe a ku Hesiboni,+ amene ali pafupi ndi chipata cha Bati-rabimu. Mphuno yako ili ngati nsanja ya Lebanoni, imene inayang’ana cha ku Damasiko.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena