Yesaya 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma tsopano Yehova wanena kuti: “Pomatha ndendende zaka zitatu,*+ ulemerero+ wa Mowabu udzatha. Iye adzachititsidwa manyazi ndipo adzakumana ndi chipwirikiti chamtundu uliwonse. Otsala mwa iye adzakhala ochepa kwambiri ndiponso opanda mphamvu.”+
14 Koma tsopano Yehova wanena kuti: “Pomatha ndendende zaka zitatu,*+ ulemerero+ wa Mowabu udzatha. Iye adzachititsidwa manyazi ndipo adzakumana ndi chipwirikiti chamtundu uliwonse. Otsala mwa iye adzakhala ochepa kwambiri ndiponso opanda mphamvu.”+