Numeri 32:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Midzi ya Ataroti,+ Diboni,+ Yazeri, Nimira,+ Hesiboni,+ Eleyale,+ Sebamu, Nebo,+ ndi Beoni,+ Yeremiya 48:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “‘Kulira kochokera ku Hesiboni+ kudzamveka ku Eleyale+ ndi ku Yahazi.+ Kulira kochokera ku Zowari+ kudzamveka ku Horonaimu+ ndi ku Egilati-selisiya.+ Madzi a ku Nimurimu+ nawonso adzawonongedwa.
34 “‘Kulira kochokera ku Hesiboni+ kudzamveka ku Eleyale+ ndi ku Yahazi.+ Kulira kochokera ku Zowari+ kudzamveka ku Horonaimu+ ndi ku Egilati-selisiya.+ Madzi a ku Nimurimu+ nawonso adzawonongedwa.