Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 21:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Koma Sihoni sanalole kuti Aisiraeli adzere m’dziko lake.+ M’malomwake, iye anasonkhanitsa anthu ake onse n’kupita kukamenyana ndi Aisiraeli m’chipululumo. Anakafika ku Yahazi,+ kumene anayamba kumenyana ndi Aisiraeli.

  • Deuteronomo 2:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Sihoni atatuluka pamodzi ndi anthu ake onse kudzamenyana nafe nkhondo ku Yahazi,+

  • Oweruza 11:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Koma Sihoni sanakhulupirire kuti Aisiraeli akufuna kungodutsa m’dziko lake. Choncho Sihoni anasonkhanitsa anthu ake onse pamodzi ndi kumanga misasa ku Yahazi+ n’kuyamba kumenyana ndi Aisiraeliwo.+

  • Yesaya 15:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Hesiboni ndi Eleyale+ akulira mofuula. Mawu awo amveka mpaka ku Yahazi.+ N’chifukwa chake amuna onyamula zida a ku Mowabu akungofuula. Mitima yawo ikuchita mantha kwambiri.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena