Numeri 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma Sihoni sanalole kuti Aisiraeli adzere m’dziko lake.+ M’malomwake, iye anasonkhanitsa anthu ake onse n’kupita kukamenyana ndi Aisiraeli m’chipululumo. Anakafika ku Yahazi,+ kumene anayamba kumenyana ndi Aisiraeli. Oweruza 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Sihoni sanakhulupirire kuti Aisiraeli akufuna kungodutsa m’dziko lake. Choncho Sihoni anasonkhanitsa anthu ake onse pamodzi ndi kumanga misasa ku Yahazi+ n’kuyamba kumenyana ndi Aisiraeliwo.+
23 Koma Sihoni sanalole kuti Aisiraeli adzere m’dziko lake.+ M’malomwake, iye anasonkhanitsa anthu ake onse n’kupita kukamenyana ndi Aisiraeli m’chipululumo. Anakafika ku Yahazi,+ kumene anayamba kumenyana ndi Aisiraeli.
20 Koma Sihoni sanakhulupirire kuti Aisiraeli akufuna kungodutsa m’dziko lake. Choncho Sihoni anasonkhanitsa anthu ake onse pamodzi ndi kumanga misasa ku Yahazi+ n’kuyamba kumenyana ndi Aisiraeliwo.+