9 N’chifukwa chake ndidzalirire mtengo wa mpesa wa ku Sibima ngati mmene ndinachitira polirira Yazeri.+ Ndidzakunyowetsa kwambiri ndi misozi yanga iwe Hesiboni+ ndi Eleyale,+ chifukwa chakuti kufuula kwakugwera m’chilimwe ndi pa nthawi ya zokolola zako.+