Yeremiya 48:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “‘Iwe mtengo wa mpesa wa ku Sibima+ ndidzakulirira kuposa mmene ndingalirire Yazeri.+ Mphukira zako zosangalala zawoloka nyanja. Zafika kunyanja, ku Yazeri.+ Munthu wofunkha waukira zipatso zako za m’chilimwe*+ ndi mphesa zimene wakolola.+
32 “‘Iwe mtengo wa mpesa wa ku Sibima+ ndidzakulirira kuposa mmene ndingalirire Yazeri.+ Mphukira zako zosangalala zawoloka nyanja. Zafika kunyanja, ku Yazeri.+ Munthu wofunkha waukira zipatso zako za m’chilimwe*+ ndi mphesa zimene wakolola.+