Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 48:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Iwe mtengo wa mpesa wa ku Sibima+

      Ndidzakulirira kuposa mmene ndingalirire Yazeri.+

      Mphukira zako zosangalala zawoloka nyanja.

      Zafika kunyanja, ku Yazeri.

      Munthu wowononga wabwera kudzawononga

      Zipatso zako zamʼchilimwe* ndi mphesa zimene wakolola.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena