Yeremiya 40:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ine ndikhala ku Mizipa+ kuno kuti ndizikuimirani kwa Akasidi amene adzabwera kwa ife. Koma inu, sonkhanitsani vinyo,+ zipatso za m’chilimwe* ndi mafuta ndi kuziika m’ziwiya zanu ndipo muzikhala m’mizinda imene mwaitenga kukhala yanu.”
10 Ine ndikhala ku Mizipa+ kuno kuti ndizikuimirani kwa Akasidi amene adzabwera kwa ife. Koma inu, sonkhanitsani vinyo,+ zipatso za m’chilimwe* ndi mafuta ndi kuziika m’ziwiya zanu ndipo muzikhala m’mizinda imene mwaitenga kukhala yanu.”