Numeri 21:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pamenepo Mose anatumiza anthu ena kuti akazonde mzinda wa Yazeri.+ Atatero, Aisiraeliwo analanda midzi yozungulira mzindawo, n’kupitikitsa Aamori omwe anali kukhalamo.+ Numeri 32:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Atiroti-sofani, Yazeri,+ Yogebeha,+ Yoswa 21:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Hesiboni+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso Yazeri+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse pamodzi inalipo mizinda inayi.
32 Pamenepo Mose anatumiza anthu ena kuti akazonde mzinda wa Yazeri.+ Atatero, Aisiraeliwo analanda midzi yozungulira mzindawo, n’kupitikitsa Aamori omwe anali kukhalamo.+
39 Hesiboni+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso Yazeri+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse pamodzi inalipo mizinda inayi.