Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 32:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Tsopano ana a Rubeni+ ndi ana a Gadi+ anakhala ndi ziweto zambiri, zankhaninkhani. Iwo anayamba kusirira dziko la Yazeri+ ndi la Giliyadi, ndipo deralo linalidi malo abwino a ziweto.

  • Yoswa 13:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Gawo lawo linayambira kumzinda wa Yazeri,+ mizinda yonse ya ku Giliyadi,+ ndi hafu ya dziko la ana a Amoni,+ mpaka kukafika ku Aroweli+ kufupi ndi Raba.+

  • Yesaya 16:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 chifukwa minda ya m’mapiri ya ku Hesiboni+ yafota. Eni ake a mitundu ya anthu athyola nthambi za mitengo ya mpesa ya ku Sibima+ zodzaza ndi mphesa zakupsa. Nthambizo zinafika mpaka ku Yazeri.+ Zinafika mpaka kuchipululu. Mphukira zake zinasiyidwa kuti zizingodzikulira pazokha. Zinafika mpaka kunyanja.

  • Yeremiya 48:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 “‘Iwe mtengo wa mpesa wa ku Sibima+ ndidzakulirira kuposa mmene ndingalirire Yazeri.+ Mphukira zako zosangalala zawoloka nyanja. Zafika kunyanja, ku Yazeri.+ Munthu wofunkha waukira zipatso zako za m’chilimwe*+ ndi mphesa zimene wakolola.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena