Yesaya 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chifukwa minda yamʼmapiri ya ku Hesiboni+ yafota,Chimodzimodzinso mitengo ya mpesa ya ku Sibima,+Olamulira anthu a mitundu ina apondaponda nthambi zake zofiira kwambiri.*Nthambizo zinafika mpaka ku Yazeri,+Zinafika mpaka kuchipululu. Mphukira zake zinakula mpaka zinafika kunyanja. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:8 Yesaya 1, tsa. 193
8 Chifukwa minda yamʼmapiri ya ku Hesiboni+ yafota,Chimodzimodzinso mitengo ya mpesa ya ku Sibima,+Olamulira anthu a mitundu ina apondaponda nthambi zake zofiira kwambiri.*Nthambizo zinafika mpaka ku Yazeri,+Zinafika mpaka kuchipululu. Mphukira zake zinakula mpaka zinafika kunyanja.