Numeri 21:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pamenepo Mose anatumiza anthu ena kuti akazonde mzinda wa Yazeri.+ Atatero, Aisiraeliwo analanda midzi yozungulira mzindawo, n’kupitikitsa Aamori omwe anali kukhalamo.+ Yoswa 13:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Gawo lawo linayambira kumzinda wa Yazeri,+ mizinda yonse ya ku Giliyadi,+ ndi hafu ya dziko la ana a Amoni,+ mpaka kukafika ku Aroweli+ kufupi ndi Raba.+
32 Pamenepo Mose anatumiza anthu ena kuti akazonde mzinda wa Yazeri.+ Atatero, Aisiraeliwo analanda midzi yozungulira mzindawo, n’kupitikitsa Aamori omwe anali kukhalamo.+
25 Gawo lawo linayambira kumzinda wa Yazeri,+ mizinda yonse ya ku Giliyadi,+ ndi hafu ya dziko la ana a Amoni,+ mpaka kukafika ku Aroweli+ kufupi ndi Raba.+