Oweruza 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndiyeno monga mwa masiku onse, iwo analowa m’munda n’kuyamba kukolola ndi kuponda mphesa za m’minda yawo ndi kuchita chikondwerero.+ Kenako analowa m’nyumba ya mulungu wawo,+ ndipo anadya ndi kumwa+ ndi kutemberera+ Abimeleki.
27 Ndiyeno monga mwa masiku onse, iwo analowa m’munda n’kuyamba kukolola ndi kuponda mphesa za m’minda yawo ndi kuchita chikondwerero.+ Kenako analowa m’nyumba ya mulungu wawo,+ ndipo anadya ndi kumwa+ ndi kutemberera+ Abimeleki.