Yesaya 48:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ayi, inu simunamve+ kapena kudziwa zimenezi,Ndipo mʼmbuyomu makutu anu anali osatseguka, Chifukwa ndikudziwa kuti inu ndi achinyengo,+Ndipo kuyambira pamene munabadwa mumatchedwa wochimwa.+ Yeremiya 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 ‘Ndithudi, mofanana ndi mkazi amene amasiya mwamuna wake mwachinyengo, inunso a mʼnyumba ya Isiraeli mwandichitira zachinyengo,’+ akutero Yehova.” Hoseya 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Akhala osakhulupirika kwa Yehova,+Chifukwa abereka ana achilendo. Tsopano mwezi udzawadya* limodzi ndi zinthu zawo.* Hoseya 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma iwo, mofanana ndi anthu wamba, aphwanya pangano.+ Kumeneko andichitira zosakhulupirika.
8 Ayi, inu simunamve+ kapena kudziwa zimenezi,Ndipo mʼmbuyomu makutu anu anali osatseguka, Chifukwa ndikudziwa kuti inu ndi achinyengo,+Ndipo kuyambira pamene munabadwa mumatchedwa wochimwa.+
20 ‘Ndithudi, mofanana ndi mkazi amene amasiya mwamuna wake mwachinyengo, inunso a mʼnyumba ya Isiraeli mwandichitira zachinyengo,’+ akutero Yehova.”
7 Akhala osakhulupirika kwa Yehova,+Chifukwa abereka ana achilendo. Tsopano mwezi udzawadya* limodzi ndi zinthu zawo.*