Yeremiya 23:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mobwerezabwereza iwo akuuza anthu amene sakundilemekeza kuti,‘Yehova wanena kuti: “Inu mudzakhala pa mtendere.”’+ Ndipo aliyense amene amatsatira mtima wake woipawo akumuuza kuti,‘Tsoka silidzakugwerani.’+
17 Mobwerezabwereza iwo akuuza anthu amene sakundilemekeza kuti,‘Yehova wanena kuti: “Inu mudzakhala pa mtendere.”’+ Ndipo aliyense amene amatsatira mtima wake woipawo akumuuza kuti,‘Tsoka silidzakugwerani.’+