-
Yesaya 59:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Maganizo awo ndi maganizo oipa.
Zonse zimene amachita zimakhala zowononga ndiponso zobweretsa mavuto.+
-
-
Mateyu 23:34, 35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Pa chifukwa chimenechi, ndikukutumizirani aneneri,+ anthu anzeru ndi aphunzitsi.+ Ena a iwo mudzawapha+ nʼkuwapachika pamtengo ndipo ena mudzawakwapula+ mʼmasunagoge mwanu ndi kuwazunza+ mumzinda ndi mzinda, 35 kuti magazi onse a anthu olungama amene anakhetsedwa padziko lapansi abwere pa inu. Kuyambira magazi a Abele wolungama+ mpaka magazi a Zekariya mwana wa Barakiya, amene inu munamupha pakati pa nyumba yopatulika ndi guwa lansembe.+
-