Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Choncho mudzadya ana anu aamuna ndi ana anu aakazi.+

  • Deuteronomo 28:53
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 53 Zikadzatero mudzadya ana anu omwe,* mnofu wa ana anu aamuna ndi ana anu aakazi+ amene Yehova Mulungu wanu wakupatsani, chifukwa cha mavuto oopsa amene mudzakumane nawo adani anu akadzakuzungulirani.

  • Maliro 2:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Inu Yehova, yangʼanani kuti muone amene mwamulanga mwaukali.

      Kodi azimayi azidya ana awo amene* abereka, ana awo athanzi?+

      Kapena kodi ansembe ndi aneneri aziphedwa mʼmalo opatulika a Yehova?+

  • Maliro 4:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Azimayi amene amakhala achifundo, aphika ana awo ndi manja awo.+

      Anawo akhala chakudya chawo pa nthawi yachisoni pamene mwana wamkazi wa anthu anga wawonongedwa.+

  • Ezekieli 5:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Choncho azibambo amene ali mumzindawo adzadya ana awo+ ndipo ana adzadya abambo awo. Ine ndidzakulanga ndipo anthu ako onse otsala ndidzawabalalitsira kumbali zonse.”’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena